Aroma 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera. 1 Akorinto 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chilichonse chogulitsidwa pamsika wa nyama muzidya+ popanda kufunsa mafunso, poopera chikumbumtima+ chanu,
17 Pakuti ufumu wa Mulungu+ si kudya ndi kumwa ayi,+ koma chilungamo,+ mtendere+ ndi chimwemwe+ zobwera ndi mzimu woyera.
25 Chilichonse chogulitsidwa pamsika wa nyama muzidya+ popanda kufunsa mafunso, poopera chikumbumtima+ chanu,