Deuteronomo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Yehova anadziphatika kwa makolo anu ndi kuwakonda, moti anasankha ana awo obadwa m’mbuyo mwawo,+ inuyo, pakati pa anthu onse monga mmene zilili lero. Salimo 105:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu mbewu ya Abulahamu mtumiki wake,+Inu ana a Yakobo, osankhidwa mwapadera.+
15 Koma Yehova anadziphatika kwa makolo anu ndi kuwakonda, moti anasankha ana awo obadwa m’mbuyo mwawo,+ inuyo, pakati pa anthu onse monga mmene zilili lero.