Salimo 105:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu mbadwa* za Abulahamu mtumiki wake,+Inu ana a Yakobo, osankhidwa ake.+