Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe komanso mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa Aisiraeli.”

  • Yesaya 41:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+

      Iwe Yakobo, amene ndakusankha,+

      Mbadwa* ya mnzanga Abulahamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena