Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni+ ndi choonadi. Mawu+ anu ndiwo choonadi.+ 1 Akorinto 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+ 1 Atesalonika 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu sanatiitane mwa kulekerera zodetsa, koma kuti tikhale oyera.+
11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+