Yohane 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+ Aroma 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+ Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+
44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+
30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+
4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+