Yesaya 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+
4 Ndani wachita zimenezi,+ kuitana mibadwo kuyambira pa chiyambi?+ “Ndineyo Yehova, Woyamba,+ ndipo ndidzakhala chimodzimodzi ngakhale kwa omalizira.”+