Yesaya 41:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse pamodzi aone, adziwe, amve, ndiponso azindikire, kuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi, ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+ Yeremiya 31:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+
20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse pamodzi aone, adziwe, amve, ndiponso azindikire, kuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi, ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+
34 “Munthu sadzaphunzitsanso mnzake kapena m’bale wake+ kuti, ‘Mum’dziwe Yehova!’+ pakuti aliyense wa iwo adzandidziwa, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu,”+ watero Yehova. “Ine ndidzawakhululukira zolakwa zawo ndipo machimo awo sindidzawakumbukiranso.”+