Salimo 109:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo adziwe kuti ili ndi dzanja lanu.+Adziwe kuti inu Yehova mwachita zimenezi.+ Ezekieli 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa kumayiko ena n’kuwabwezanso kudziko lawo onse pamodzi.+ Kumayikowo ndidzatengako Aisiraeli onse moti sindidzasiyako aliyense.+
28 “‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa kumayiko ena n’kuwabwezanso kudziko lawo onse pamodzi.+ Kumayikowo ndidzatengako Aisiraeli onse moti sindidzasiyako aliyense.+