Ezekieli 34:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Iwo adzadziwa kuti ine, Yehova Mulungu wawo, ndili nawo limodzi+ ndiponso kuti iwowo, a nyumba ya Isiraeli ndi anthu anga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’+
30 ‘Iwo adzadziwa kuti ine, Yehova Mulungu wawo, ndili nawo limodzi+ ndiponso kuti iwowo, a nyumba ya Isiraeli ndi anthu anga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’+