2 Mafumu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo. Yeremiya 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo. Yeremiya 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+
22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo.
14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.
2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+