Yeremiya 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Yeremiya anapita ku Mizipa+ kukakhala ndi Gedaliya+ mwana wa Ahikamu pakati pa anthu amene anatsala m’dzikolo.
6 Chotero Yeremiya anapita ku Mizipa+ kukakhala ndi Gedaliya+ mwana wa Ahikamu pakati pa anthu amene anatsala m’dzikolo.