2 Mafumu 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako mfumuyo inalamula wansembe Hilikiya, Ahikamu+ mwana wa Safani, Akibori mwana wa Mikaya, Safani mlembi, ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti: Yeremiya 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anali kuteteza Yeremiya kuti anthu asamuphe.+
12 Kenako mfumuyo inalamula wansembe Hilikiya, Ahikamu+ mwana wa Safani, Akibori mwana wa Mikaya, Safani mlembi, ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti: