1 Mafumu 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+ Machitidwe 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Chotero analamula asilikali+ kuti apite komweko kuti akamuchotse pakati pawo ndi kumubweretsa kumpanda wa asilikali.+
4 Choncho pamene Yezebeli+ anapha aneneri a Yehova,+ Obadiya anatenga aneneri 100 n’kuwagawa m’magulu awiri, gulu lililonse aneneri 50. Atatero anakawabisa kuphanga ndipo anali kuwapatsa mkate ndi madzi.)+
10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Chotero analamula asilikali+ kuti apite komweko kuti akamuchotse pakati pawo ndi kumubweretsa kumpanda wa asilikali.+