2 Mafumu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo. Yeremiya 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anali kuteteza Yeremiya kuti anthu asamuphe.+
22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo.