Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Tsopano m’mwezi wa 7,+ Isimaeli+ mwana wa Netaniya mwana wa Elisama, anapita kwa Gedaliya pamodzi ndi amuna 10. Isimaeli anali wa m’banja lachifumu. Iye pamodzi ndi amunawo anapha Gedaliya+ ndi Ayuda ndiponso Akasidi amene anali naye pamodzi ku Mizipa.+

  • Yeremiya 39:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.

  • Yeremiya 41:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena