Yeremiya 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+
2 Ndiyeno Isimaeli mwana wa Netaniya ndi amuna 10 amene anali naye ananyamuka ndi kukapha ndi lupanga Gedaliya mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani. Choncho Isimaeli anapha munthu amene mfumu ya Babulo inamuika kuti azilamulira dzikolo.+