2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga. 2 Mbiri 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako mfumuyo inalamula Hilikiya,+ Ahikamu+ mwana wa Safani, Abidoni mwana wa Mika, Safani+ mlembi,+ ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti:
8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.
20 Kenako mfumuyo inalamula Hilikiya,+ Ahikamu+ mwana wa Safani, Abidoni mwana wa Mika, Safani+ mlembi,+ ndi Asaya+ mtumiki wa mfumu, kuti: