2 Mafumu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo. Yeremiya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya ana a Amoni+ watumiza Isimaeli+ mwana wa Netaniya+ kuti adzakuphe?” Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanakhulupirire zimenezo.+
22 Ndiyeno Nebukadinezara mfumu ya Babulo, anasankha Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani,+ kuti akhale mtsogoleri wa anthu+ amene anatsala m’dziko la Yuda, amene mfumuyo inawasiya mmenemo.
14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya ana a Amoni+ watumiza Isimaeli+ mwana wa Netaniya+ kuti adzakuphe?” Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanakhulupirire zimenezo.+