-
Yeremiya 41:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako Isimaeli anagwira anthu onse otsala, ana aakazi a mfumu,+ amene anali ku Mizipa.+ Anagwiranso anthu ena onse otsala ku Mizipa+ amene Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawapereka kwa Gedaliya mwana wa Ahikamu+ kuti aziwayang’anira. Chotero Isimaeli mwana wa Netaniya anawagwira ndipo ananyamuka kuti awolokere nawo kudziko la ana a Amoni.+
-