Yeremiya 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Ayuda onse anayamba kubwerera kuchokera kumadera onse kumene anathawira. Anali kubwera m’dziko la Yuda kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Iwo anasonkhanitsa vinyo ndi zipatso za m’chilimwe zochuluka kwambiri.
12 Ndiyeno Ayuda onse anayamba kubwerera kuchokera kumadera onse kumene anathawira. Anali kubwera m’dziko la Yuda kwa Gedaliya ku Mizipa.+ Iwo anasonkhanitsa vinyo ndi zipatso za m’chilimwe zochuluka kwambiri.