Yeremiya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya ana a Amoni+ watumiza Isimaeli+ mwana wa Netaniya+ kuti adzakuphe?” Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanakhulupirire zimenezo.+
14 Iwo anauza Gedaliya kuti: “Kodi sukudziwa kuti Baalisi mfumu ya ana a Amoni+ watumiza Isimaeli+ mwana wa Netaniya+ kuti adzakuphe?” Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu sanakhulupirire zimenezo.+