Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso muzichita chikondwerero cha zokolola, chokondwerera zipatso za ntchito ya manja anu zoyamba kucha+ zimene munabzala m’munda.+ Muzichitanso chikondwerero cha kututa kumapeto kwa chaka, pamene mututa zipatso za manja anu, zam’munda.+

  • 1 Samueli 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Sauli anafunsa mtumiki wakeyo kuti: “Ndiye tikapita kumeneko tikam’patsa chiyani?+ Tilibe mphatso+ imene tingapatse munthu wa Mulungu woonayo, chifukwanso mkate watha m’zotengera zathu. Tili ndi chiyani?”

  • Agalatiya 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Komanso, aliyense amene akuphunzitsidwa mawuwo+ agawane+ zinthu zonse zabwino ndi amene akumuphunzitsayo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena