Numeri 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inuyo ndi a m’nyumba zanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa ndizo malipiro anu pa utumiki umene muzichita m’chihema chokumanako.+ Mateyu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ 1 Akorinto 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+
31 Inuyo ndi a m’nyumba zanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa ndizo malipiro anu pa utumiki umene muzichita m’chihema chokumanako.+
10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+