Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 18:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Inuyo ndi a m’nyumba zanu muzidya zimenezo pamalo alionse, chifukwa ndizo malipiro anu pa utumiki umene muzichita m’chihema chokumanako.+

  • Maliko 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso, anawalangiza kuti asanyamule kanthu pa ulendowo kupatulapo ndodo yokha basi. Anawalangiza kuti asatenge mkate, thumba la chakudya,+ kapena ndalama m’zikwama zawo,+

  • Luka 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye anawauza kuti: “Musanyamule kanthu pa ulendowu, musatenge ndodo, kapena thumba la chakudya, kapena mkate, kapena ndalama zasiliva, kapena kutenga malaya awiri amkati.+

  • Luka 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+

  • 1 Akorinto 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+

  • 1 Timoteyo 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pakuti lemba limati: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Komanso limati: “Wantchito ayenera kulandira malipiro ake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena