Mateyu 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+ Maliko 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso, anawalangiza kuti asanyamule kanthu pa ulendowo kupatulapo ndodo yokha basi. Anawalangiza kuti asatenge mkate, thumba la chakudya,+ kapena ndalama m’zikwama zawo,+ Luka 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatenge chikwama cha ndalama, thumba la chakudya,+ kapena nsapato. Ndipo musamachedwe mukamapereka moni panjira.+
10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
8 Komanso, anawalangiza kuti asanyamule kanthu pa ulendowo kupatulapo ndodo yokha basi. Anawalangiza kuti asatenge mkate, thumba la chakudya,+ kapena ndalama m’zikwama zawo,+
4 Musatenge chikwama cha ndalama, thumba la chakudya,+ kapena nsapato. Ndipo musamachedwe mukamapereka moni panjira.+