Oweruza 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Tiloleni tikuchedwetseni pang’ono, kuti tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+ Oweruza 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake+ ndipo anapatsa abulu ake aja chakudya.+ Ndiyeno anasamba mapazi awo+ n’kuyamba kudya ndi kumwa.
15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Tiloleni tikuchedwetseni pang’ono, kuti tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+
21 Atatero anatengera Mlevi uja kunyumba kwake+ ndipo anapatsa abulu ake aja chakudya.+ Ndiyeno anasamba mapazi awo+ n’kuyamba kudya ndi kumwa.