Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”

  • Genesis 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako, Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, n’kutengako ng’ombe yaing’ono yamphongo yonona. Atatero, anaipereka kwa wantchito wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.+

  • Oweruza 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chonde musachoke, kufikira nditabwera+ ndi kukupatsani mphatso yanga.”+ Choncho iye anati: “Ineyo ndikhalabe pompano kufikira utabweranso.”

  • Aheberi 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Musaiwale kuchereza alendo,+ pakuti potero, ena anachereza angelo mosadziwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena