Genesis 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anati: “Yehova, ngati mungandikomere mtima, chonde, musangondipitirira ine kapolo wanu.+ Genesis 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya. Oweruza 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Tiloleni tikuchedwetseni pang’ono, kuti tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+
3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya.
15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Tiloleni tikuchedwetseni pang’ono, kuti tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+