Oweruza 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chonde musachoke, mpaka nditabwera nʼkukupatsani mphatso.”+ Choncho iye anati: “Ndikhalabe pompano mpaka utabweranso.”
18 Chonde musachoke, mpaka nditabwera nʼkukupatsani mphatso.”+ Choncho iye anati: “Ndikhalabe pompano mpaka utabweranso.”