Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Popeza mwadzera njira yodutsa kwa kapolo wanu, mundilole ndikukonzereni kachakudya kuti mutsitsimutse mitima yanu.+ Mukatero mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”

  • Oweruza 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Gidiyoni analowa m’nyumba ndi kuphika nyama ya mwana wa mbuzi.+ Anatenganso ufa wokwana muyezo umodzi wa efa* ndi kupanga mikate yopanda chofufumitsa.+ Atatero, anatenga nyamayo ndi kuiika m’dengu, ndipo msuzi anauika mumphika. Kenako, anatenga zinthu zimenezi ndi kukamupatsa mngelo uja pansi pa mtengo waukulu uja.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena