Genesis 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako, Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, n’kutengako ng’ombe yaing’ono yamphongo yonona. Atatero, anaipereka kwa wantchito wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.+
7 Kenako, Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, n’kutengako ng’ombe yaing’ono yamphongo yonona. Atatero, anaipereka kwa wantchito wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.+