1 Mafumu 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Isiraeli inawatsatira n’kumapha mahatchi ndi kuwononga magaleta+ awo, ndipo inapha Asiriya ochuluka zedi.
21 Mfumu ya Isiraeli inawatsatira n’kumapha mahatchi ndi kuwononga magaleta+ awo, ndipo inapha Asiriya ochuluka zedi.