Yoswa 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ pakuti mawa pa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundula,*+ ndipo magaleta awo udzawatentha ndi moto.”+
6 Pamenepo Yehova anauza Yoswa kuti: “Usawaope,+ pakuti mawa pa nthawi ngati yomwe ino, ndidzawapereka onsewo kuti aphedwe ndi Aisiraeli. Mahatchi awo udzawapundula,*+ ndipo magaleta awo udzawatentha ndi moto.”+