Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ Yoswa 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake Yoswa anachita zimene Yehova anamuuza. Mahatchi awo anawapundula,+ ndipo magaleta awo anawatentha ndi moto.+ 2 Samueli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi amuna 20,000 oyenda pansi+ a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula*+ mahatchi onse a magaleta+ kusiyapo mahatchi a magaleta okwana 100.
16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
9 Pambuyo pake Yoswa anachita zimene Yehova anamuuza. Mahatchi awo anawapundula,+ ndipo magaleta awo anawatentha ndi moto.+
4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi amuna 20,000 oyenda pansi+ a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula*+ mahatchi onse a magaleta+ kusiyapo mahatchi a magaleta okwana 100.