2 Mafumu 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Elisa anapita ku Damasiko.+ Kumeneko Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya inali kudwala. Choncho mfumuyo inauzidwa kuti: “Munthu wa Mulungu woona uja+ wafika kuno.”
7 Kenako Elisa anapita ku Damasiko.+ Kumeneko Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya inali kudwala. Choncho mfumuyo inauzidwa kuti: “Munthu wa Mulungu woona uja+ wafika kuno.”