-
1 Mafumu 20:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Tsopano Beni-hadadi anauza Ahabu kuti: “Ndibweza mizinda+ imene bambo anga analanda bambo anu, ndipo inuyo mutenga misewu ku Damasiko mofanana ndi mmene bambo anga anatengera misewu ku Samariya.”
Ahabu anayankha kuti: “Tikapanga pangano+ loti udzachitadi zimenezi, ndikusiya kuti uzipita kwanu.”
Atatero anachita naye pangano ndipo anamuuza kuti azipita kwawo.
-