2 Mbiri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu. 2 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+
7 Pa nthawi imeneyo, wamasomphenya* Haneni+ anapita kwa Asa mfumu ya Yuda n’kumuuza kuti: “Chifukwa chakuti munadalira mfumu ya Siriya,+ osadalira Yehova Mulungu wanu,+ gulu lankhondo la mfumu ya Siriya lathawa m’manja mwanu.
9 Pajatu maso a Yehova+ akuyendayenda padziko lonse lapansi+ kuti aonetse mphamvu zake kwa anthu amene mtima wawo+ uli wathunthu kwa iye. Mwachita zopusa+ pankhani imeneyi, chifukwa kuyambira tsopano anthu azichita nanu nkhondo.”+