2 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+ Aheberi 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+
5 Iye anadalira Yehova Mulungu wa Isiraeli.+ Panalibenso mfumu ina yofanana naye pamafumu onse a Yuda+ amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa.+
12 Choncho, chifukwa chakuti tili ndi mtambo wa mboni+ waukulu chonchi wotizungulira, tiyeninso tivule cholemera chilichonse+ ndi tchimo limene limatikola mosavuta lija.+ Ndipo tithamange mopirira+ mpikisano+ umene atiikirawu.+