Akolose 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani: mwina wina angakugwireni+ ngati nyama, mwa nzeru za anthu+ ndi chinyengo chopanda pake,+ malinga ndi miyambo ya anthu, malinganso ndi mfundo zimene zili maziko a moyo wa m’dzikoli,+ osati malinga ndi Khristu, 1 Timoteyo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+ Aheberi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+
8 Samalani: mwina wina angakugwireni+ ngati nyama, mwa nzeru za anthu+ ndi chinyengo chopanda pake,+ malinga ndi miyambo ya anthu, malinganso ndi mfundo zimene zili maziko a moyo wa m’dzikoli,+ osati malinga ndi Khristu,
9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+
12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+