Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano mawu a Yehova otsutsana ndi Basa anafikira Yehu+ mwana wa Haneni,+ kuti:

  • 2 Mbiri 19:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano Yehu+ mwana wa Haneni+ wamasomphenya,+ anapita kukaonekera kwa Mfumu Yehosafati ndipo anaifunsa kuti: “Kodi chithandizo chiyenera kuperekedwa+ kwa oipa, ndipo kodi muyenera kukonda anthu odana+ ndi Yehova?+ Chifukwa cha zimenezi Yehova wakukwiyirani.+

  • 2 Mbiri 20:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nkhani zina zokhudza Yehosafati, zoyambirira ndi zomalizira, zinalembedwa m’mawu a Yehu+ mwana wa Haneni.+ Mawuwa analembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena