2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:19 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 26
19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+