Genesis 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+ 2 Mafumu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 mpaka Yehova anachotsa Isiraeli pamaso pake+ monga momwe ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Isiraeli anachoka m’dziko lake n’kupita ku Asuri, ndipo ali komweko mpaka lero.+
14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+
23 mpaka Yehova anachotsa Isiraeli pamaso pake+ monga momwe ananenera kudzera mwa atumiki ake onse, aneneri.+ Choncho Isiraeli anachoka m’dziko lake n’kupita ku Asuri, ndipo ali komweko mpaka lero.+