Deuteronomo 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikananena kuti: “Ndidzawabalalitsa,+Ndidzachititsa anthu kuti asatchule n’komwe za iwo,”+ 2 Mafumu 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yehova anakomera mtima+ Aisiraeli ndi kuwachitira chifundo+ ndipo anatembenukira kwa iwo chifukwa cha pangano lake+ ndi Abulahamu,+ Isaki,+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga+ ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero. 2 Mafumu 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Yehova anati: “Yuda+ nayenso ndim’chotsa pamaso panga+ monga mmene ndinachotsera Isiraeli,+ ndipo ndithu ndidzakana ngakhale mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala pamenepo.’”+
23 Koma Yehova anakomera mtima+ Aisiraeli ndi kuwachitira chifundo+ ndipo anatembenukira kwa iwo chifukwa cha pangano lake+ ndi Abulahamu,+ Isaki,+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga+ ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero.
27 Koma Yehova anati: “Yuda+ nayenso ndim’chotsa pamaso panga+ monga mmene ndinachotsera Isiraeli,+ ndipo ndithu ndidzakana ngakhale mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala pamenepo.’”+