Salimo 145:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+ 2 Akorinto 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu ndi Atate+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Tate wachifundo chachikulu+ ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse,+ Aefeso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+
8 Yehova ndi wachisomo ndi wachifundo,+Wosakwiya msanga ndi wosonyeza kukoma mtima kosatha komanso kwakukulu.+
3 Atamandike Mulungu ndi Atate+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Tate wachifundo chachikulu+ ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse,+
4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+