Deuteronomo 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+ 2 Mafumu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi zinachitikira Yuda molamulidwa ndi Yehova, kuti achotse+ dzikolo pamaso pake chifukwa cha machimo a Manase,+ malinga ndi zonse zimene anachita,
28 Choncho Yehova anawazula m’dziko lawo atapsa mtima,+ ali ndi ukali ndiponso mkwiyo waukulu n’kuwataya m’dziko lina monga mmene zilili lero.’+
3 Zimenezi zinachitikira Yuda molamulidwa ndi Yehova, kuti achotse+ dzikolo pamaso pake chifukwa cha machimo a Manase,+ malinga ndi zonse zimene anachita,