Yeremiya 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mphepo idzaweta abusa ako onse+ ndipo anthu onse amene akukukonda kwambiri adzatengedwa kupita ku ukapolo.+ Pa nthawi imeneyo udzachita manyazi ndipo udzanyazitsidwadi chifukwa cha tsoka limene lidzakugwere.+
22 Mphepo idzaweta abusa ako onse+ ndipo anthu onse amene akukukonda kwambiri adzatengedwa kupita ku ukapolo.+ Pa nthawi imeneyo udzachita manyazi ndipo udzanyazitsidwadi chifukwa cha tsoka limene lidzakugwere.+