Miyambo 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aliyense wochenjera amachita zinthu mozindikira,+ koma wopusa amafalitsa uchitsiru.+ Miyambo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+
2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+ koma pakamwa pa zitsiru pamasefukira mawu opusa.+