Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 45:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Mtima wanga wagalamuka chifukwa cha nkhani yosangalatsa.+

      Ine ndikuti: “Nyimbo yangayi ikunena za mfumu.”+

      Lilime langa likhale ngati cholembera+ cha wokopera malemba waluso.+

  • Miyambo 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mtima wa munthu wanzeru umamuchititsa kuti asonyeze kuzindikira ndi pakamwa pake,+ ndipo umachititsa milomo yake kutulutsa mawu okopa.+

  • Mlaliki 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mawu a m’kamwa mwa munthu wanzeru amakhala osangalatsa,+ koma milomo ya munthu wopusa imamuwononga.+

  • Yesaya 50:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino+ kuti ndidziwe mmene ndingamuyankhire munthu wotopa.+ Iye amandidzutsa m’mawa uliwonse. Amandidzutsa kuti makutu anga amve ngati anthu ophunzitsidwa bwino.+

  • Yohane 7:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Alondawo anayankha kuti: “Palibe munthu amene analankhulapo ngati iyeyu n’kale lonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena