Salimo 37:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+ Miyambo 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+ Miyambo 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti n’chinthu chosangalatsa kuti uzisunge mumtima mwako,+ kuti zikhazikike pamilomo yako.+ Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+
17 Tchera khutu lako ndi kumva mawu a anthu anzeru,+ kuti ulandire ndi mtima wonse nzeru zochokera kwa ine.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+